Udzu
Grass
e.g.
Udzu umapangitsa pamalo kuti pazioneka bwino.
en
Grass makes the place look nice.
By
Joseph banda

Udzu
Weed
e.g.
Udzu ndi mbewu yosafunika munda.
en
Weed is unwanted plant in the field.
By
Joseph banda
